Masalmo 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine, mwa kucuruka kwa cifundo canu ndidzalowa m'nyumba yanu:Ndidzagwada kuyang'ana Kacisi wanu woyera ndi kuopa Inu.

Masalmo 5

Masalmo 5:4-9