Masalmo 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akondwere onse amene athawira kwa Inu,Apfuule mokondwera kosaleka, popeza muwafungatira;Nasekere mwa Inu iwo akukonda dzina lanu.

Masalmo 5

Masalmo 5:9-12