Masalmo 49:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Koma Mulungu adzaombola moyo wanga ku mphamvu ya manda:Pakuti adzandilandira ine.

16. Usaope polemezedwa munthu,Pocuruka ulemu wa nyumba yace;

17. Pakuti pomwalira iye sadzamuka nako kanthu kali konse;Ulemu wace sutsika naye kumtsata m'mbuyo.

Masalmo 49