Masalmo 49:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aikidwa m'manda ngati nkhosa;Mbusa wao ndi imfa:Ndipo m'mawa mwace oongoka mtima adzakhala mafumu ao;Ndipo maonekedwe ao adzanyekera kumanda, kuti pokhala pace padzasowa.

Masalmo 49

Masalmo 49:9-20