Masalmo 49:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Dzamveni kuno, anthu inu nonse;Cherani khutu, inu nonse amakono,

2. Awamba ndi omveka omwe,Acuma ndi aumphawi omwe.

3. Pakamwa panga padzanena zanzeru;Ndipo cilingiriro ca mtima wanga cidzakhala ca cidziwitso.

Masalmo 49