Masalmo 44:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Tikadaiwala dzina la Mulungu wathu,Ndi kutambasulira manja athu kwa mulungu wacilendo;

21. Mulungu sakadasanthula ici kodi?Pakuti adziwa zinsinsi za mtima.

22. Koma, cifukwa ca Inu, tiphedwa tsiku lonse;Tiyesedwa ngati nkhosa zakuzipha.

Masalmo 44