Masalmo 42:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Udziweramiranji moyo wanga iwe?Ndi kuzingwa m'kati mwanga?Yembekeza Mulungu: pakuti ndidzamlemekeza tsopanonso,Ndiye cipulumutso ca nkhope yanga ndi Mulungu wanga,

Masalmo 42

Masalmo 42:4-11