Masalmo 41:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Wodala iye amene asamalira wosauka:Tsiku la tsoka Yehova adzampulumutsa: Yehova adzamsunga, nadzamsunga ndi moyo