Masalmo 40:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu, Yehova, Mulungu wanga, zodabwiza zanu mudazicita nzambiri,Ndipo zolingirira zanu za pa ife;Palibe wina wozifotokozera Inu;Ndikazisimba ndi kuzichula, Zindicurukira kuziwerenga.

Masalmo 40

Masalmo 40:1-12