Masalmo 40:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatsa Nyimbo yatsopano m'kamwa mwanga, cilemekezo ca kwa Mulungu wanga;Ambiri adzaciona, nadzaopa,Ndipo adzakhulupirira Yehova.

Masalmo 40

Masalmo 40:1-12