Masalmo 40:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga,Zocimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya;Ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandicokera mtima.

Masalmo 40

Masalmo 40:11-16