Masalmo 40:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Kuyembekeza ndayembekeza Yehova;Ndipo anandilola, namva kupfuula kwanga. Ndipo anandikweza kunditurutsa m'dzenje