Masalmo 4:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Iphani nsembe za cilungamo,Ndipo mumkhulupirire Yehova.

6. Ambiri amati, Adzationetsa cabwino ndani?Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.

7. Mwapatsa cimwemwe mumtima mwanga,Cakuposa cao m'nyengo yakucuruka dzinthu zao ndi vinyo wao.

Masalmo 4