Masalmo 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pakupfuula ine mundiyankhe, Mulungu wa cilungamo canga;Pondicepera mwandikulitsira malo:Ndicitireni cifundo, imvani pemphero langa.

2. Amuna inu, ulemu wanga udzakhala wamanyazi kufikira liti?Mudzakonda zacabe, ndi kufunafuna bodza kufikira liti?

Masalmo 4