Masalmo 39:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Imvani pemphero langa, Yehova, ndipo cherani khutu kulira kwanga;Musakhale cete pa misozi yanga:Pakuti ine ndine mlendo ndi Inu,Wosakhazikika, monga makolo anga onse.

13. Ndiloleni, kuti nditsitsimuke,Ndisanamuke ndi kukhala kuli zi.

Masalmo 39