Masalmo 39:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula cifukwa ca mphulupulu,Mukanganula kukongola kwace monga mumacita ndi kadzoce:Indedi, munthu ali yense ali cabe.

Masalmo 39

Masalmo 39:5-13