Masalmo 38:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo iwo akubwezera coipa pa cabwinoAtsutsana nane, popeza nditsata cabwino. Musanditaye, Yehova:Mulungu wanga