Masalmo 38:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo andichera misampha iwo akufuna moyo wanga;Ndipo iwo akuyesa kundicitira coipa alankhula zoononga,Nalingirira zonyenga tsiku lonse.

Masalmo 38

Masalmo 38:6-18