Masalmo 33:18-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Taonani, diso la Yehova liri pa iwo akumuopa Iye,Pa iwo akuyembekeza cifundo cace;

19. Kupulumutsa moyo wao kwa imfa,Ndi kuwasunga ndi moyo m'nyengo ya njala.

20. Moyo wathu walindira Yehova:Iye ndiye thandizo lathu ndi cikopa cathu.

21. Pakuti mtima wathu udzakondwera mwa Iye,Cifukwa takhulupirira dzina lace loyera.

22. Yehova, cifundo canu cikhale pa ife,Monga takuyembekezani Inu.

Masalmo 33