Masalmo 33:12-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Wodalitsika mtundu wa anthu umene Yehova ndiye Mulungu wao;Mtundu womwe anausankha ukhale colandira ca iye yekha.

13. Yehova apenyerera m'mwamba; Aona ana onse a anthu.

14. M'malo akhalamo Iye, amapenya pansiPa onse akukhala m'dziko lapansi;

15. Iye amene akonza mitima ya iwo onse,Amene azindikira zocita zao zonse.

Masalmo 33