Masalmo 32:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musakhale monga kavalo, kapena ngati buru, wopanda nzeru:Zomangira zao ndizo cam'kamwa ndi capamutu zakuwakokera,Pakuti ukapanda kutero sadzakuyandikiza.

Masalmo 32

Masalmo 32:8-11