Masalmo 31:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ha! kukoma kwanu ndiko kwakukuru nanga, kumene munasungira iwo akuopa Inu,Kumene munacitira iwo akukhulupirira Inu, pamaso pa ana a anthu!

Masalmo 31

Masalmo 31:12-24