Masalmo 29:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Liu la Yehova liswetsa nyama zazikazi,Ndipo lipulula nkhalango:Ndipo m'Kacisi mwace zonse ziri m'mwemo zimati, Ulemerero:

10. Yehova anakhala pa Cigumula:Inde Yehova akhala mfumu ku nthawi yomka muyaya.

11. Yehova adzapatsa anthu ace mphamvu:Yehova adzadalitsa anthu ace ndi mtendere.

Masalmo 29