Masalmo 29:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu,Perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu.

2. Perekani kwa Yehova ulemerero wa dzina lace:Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa.

Masalmo 29