Masalmo 28:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Yehova ndiye mphamvu yao,Inde mphamvu ya cipulumutso ca wodzozedwa wace.

9. Pulumutsani anthu anu, ndi kudalitsa colandira canu:Muwawetenso, ndi kuwanyamula nthawi zonse.

Masalmo 28