Masalmo 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musakumbukile zolakwa za ubwana wanga kapena zopikisana nanu:Mundikumbukile monga mwa cifundo canu,Cifukwa ca ubwino wanu, Yehova.

Masalmo 25

Masalmo 25:1-13