Masalmo 25:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova.

2. Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu,Ndisacite manyazi;Adani anga asandiseke ine.

3. Inde, onse akuyembekezera Inu sadzacita manyaziAdzacita manyazi iwo amene acita monyenga kopanda cifukwa.

Masalmo 25