Masalmo 25:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova. Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu,Ndisacite manyazi;Adani anga asandiseke