Masalmo 23:5-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga:Mwandidzoza mutu wanga mafuta; cikho canga cisefuka.

6. Inde ukoma ndi cifundo zidzanditsata masiku onse a moyo wanga:Ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse.

Masalmo 23