Masalmo 21:10-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Mudzaziononga zobala zao kuzicotsa pa dziko lapansi,Ndi mbeu zao mwa ana a anthu.

11. Pakuti anakupangirani coipa:Anapangana ciwembu, osakhoza kucicita.

12. Pakuti mudzawabweza m'mbuyo,Popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao,

13. Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu:Potero tidzayimba ndi kulemekeza cilimbiko canu.

Masalmo 21