Masalmo 20:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Iwowa anagonieka, nagwa:Koma ife tauka, ndipo takhala ciriri.

9. Yehova, pulumutsani,Mfumuyo atibvomereze tsiku lakuitana ife.

Masalmo 20