Masalmo 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'kusauka kwanga ndinaitana Yehova,Ndipo ndinakuwira Mulungu wanga;Mau anga anawamva m'Kacisi mwace,Ndipo mkuwo wanga wa pankhope pace unalowa m'makutu mwace.

Masalmo 18

Masalmo 18:4-11