Masalmo 18:48-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

48. Andipulumutsa kwa adani anga:Inde mundikweza pa iwo akundiukira ine:Mundikwatula kwa munthu waciwawa.

49. Cifukwa cace Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu,Ndipo dzina lanu ndidzaliyimbira.

50. Alanditsa mfumu yace ndi cipulumutso cacikuru:Nacitira cifundo wodzozedwa wace,Davide, ndi mbumba yace, ku nthawi zonse.

Masalmo 18