Masalmo 149:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Kumanga mafumu ao ndi maunyolo,Ndi omveka ao ndi majerejede acitsulo;

9. Kuwacitira ciweruzo colembedwaco:Ulemu wa okondedwa ace onse ndi uwu.Haleluya.

Masalmo 149