Masalmo 147:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Aciritsa osweka mtima,Namanga mabala ao.

4. Awerenga nyenyezi momwe ziri;Azicha maina zonsezi.

5. Ambuye wathu ndi wamkuru ndi wa mphamvu zambiri;Nzeru yace njosatha.

Masalmo 147