Masalmo 140:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa;Ndisungeni kwa munthu waciwawa;

2. Amene adzipanga zoipa mumtima mwao;Masiku onse amemeza nkhondo.

3. Anola lilime lao ngati njoka;Pansi pa milomo yao pali ululu wa mphiri.

Masalmo 140