Masalmo 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Waucitsiru amati mumtima mwace, Kulibe Mulungu.Acita zobvunda, acita nchito zonyansa;Kulibe wakucita bwino.

2. Yehova m'Mwamba anaweramira pa ana a anthu,Kuti aone ngati aliko wanzeru,Wakufuna Mulungu.

Masalmo 14