Masalmo 135:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Anatumiza zizindikilo ndi zodabwiza pakati pako,Aigupto iwe, Pa Farao ndi pa omtumikira onse.

10. Ndiye amene anapanda amitundu ambiri.Napha mafumu amphamvu;

11. Sihoni mfumu ya Aamori,Ndi Ogi mfumu ya Basana,Ndi maufumu onse a Kanani:

Masalmo 135