Masalmo 135:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Pakuti Yehova adzaweruza anthu ace,Koma adzaleka atumiki ace.

15. Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golidi,Nchito ya manja a anthu.

16. Pakamwa ali napo koma osalankhula;Maso ali nao, koma osapenya;

Masalmo 135