Masalmo 133:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Onani, nkokoma ndi kokondweretsa ndithuKuti abale akhale pamodzi!

2. Ndiko ngati mafuta a mtengo wace pamutu,Akutsikira ku ndebvu,Inde ku ndebvu za Aroni;Akutsikira ku mkawo wa zobvala zace

Masalmo 133