Masalmo 132:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Apo ndidzaphukitsira Davide nyanga;Ndak onzeraru wodzozedwa wanga nyali.

18. Ndidzawabvekaadani ace ndi manyaziKoma pa iyeyu korona wace adzambveka.

Masalmo 132