Masalmo 131:2-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;Ngati mwana womletsa kuyamwa amace,Moyo wanga ndiri nao ngati mwana womletsa kuyamwa.

3. Israyeli, uyembekezere Yehova,Kuyambira tsopano kufikira kosatha.

Masalmo 131