Masalmo 130:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Moyo wanga uyang'anira Ambuye,Koposa alonda matanda kuca;Inde koposa alonda matanda kuca.

7. Israyeli, uyembekezere Yehova;Cifukwa kwa Yehova kuli cifundo,Kwaonso kucurukira ciombolo.

8. Ndipo adzaombola IsrayeliKu mphulupulu zace zonse.

Masalmo 130