Masalmo 129:7-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Umene womweta sadzaza nao dzanja lace,Kapena womanga mitolo sakupatira manja.

8. Angakhale opitirirapo sanena,Dalitso la Mulungu likhale pa inu;Tikudalitsani m'dzina la Yehova.

Masalmo 129