Masalmo 129:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga,Anene tsono Israyeli;

2. Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga;Koma sanandilaka.

Masalmo 129