Masalmo 125:4-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Citirani cokoma, Yehova, iwo okhala okoma;Iwo okhala oongoka mumtima mwao. Koma iwo akupatuka kutsata njira zao