Masalmo 125:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Pakuti ndodo yacifumu ya coipa siidzapumula pa gawo la olungama;Kuti olungama asaturutse dzanja lao kucita cosalungama,

4. Citirani cokoma, Yehova, iwo okhala okoma;Iwo okhala oongoka mumtima mwao.

5. Koma iwo akupatuka kutsata njira zao zokhotakhota,Yehova adzawacotsa pamodzi ndi ocita zopanda pace.Mtendere ukhale pa Israyeli.

Masalmo 125