Masalmo 124:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Akadapanda kukhala nafe Yehova,Anene tsono Israyeli;

2. Akadapanda kukhala nafe Yehova,Pakutiukira anthu:

3. Akadatimeza amoyo,Potipsera mtima wao.

Masalmo 124