Masalmo 123:3-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Muticitire cifundo, Yehova, muticitire cifundo;Pakuti takhuta kwambiri ndi mnyozo.

4. Moyo wathu wakhuta ndithuNdi kuseka kwa iwo osasowa kanthu,Ndi mnyozo wa odzikuza.

Masalmo 123