Masalmo 122:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Cifukwa ca abale anga ndi mabwenzi anga,Ndidzanena tsopano, Mukhale mtendere mwa inu.

9. Cifukwa ca nyumba ya Yehova Mulungu wathuNdidzakufunira zokoma,

Masalmo 122